Mlaliki 7:4 - Buku Lopatulika4 Mtima wa anzeru uli m'nyumba ya maliro; koma mtima wa zitsiru uli m'nyumba ya kuseka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Mtima wa anzeru uli m'nyumba ya maliro; koma mtima wa zitsiru uli m'nyumba ya kuseka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mtima wa munthu wanzeru umalingalira kaŵirikaŵiri za imfa. Koma mtima wa munthu wopusa umalingalira za chimwemwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mtima wa munthu wanzeru nthawi zonse umalingalira za imfa, koma mitima ya zitsiru imalingalira za chisangalalo. Onani mutuwo |