Mlaliki 7:3 - Buku Lopatulika3 Chisoni chiposa kuseka; pakuti nkhope yakugwa ikonza mtima. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Chisoni chiposa kuseka; pakuti nkhope yakugwa ikonza mtima. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Chisoni nchabwino kupambana chimwemwe, chifukwa ngakhale nkhope ikhale yakugwa, mtima umathabe kutolapo nzeru. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Chisoni nʼchabwino kusiyana ndi kuseka, pakuti nkhope yakugwa ndi yabwino chifukwa imakonza mtima. Onani mutuwo |