Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 7:11 - Buku Lopatulika

11 Nzeru ili yabwino pamodzi ndi cholowa; akuona dzuwa apindula nayo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Nzeru ili yabwino pamodzi ndi cholowa; akuona dzuwa apindula nayo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Nzeru nzabwino ngati choloŵa chomwe, zimapindulitsa wamoyo aliyense pansi pano.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Nzeru ngati cholowa, ndi chinthu chabwino ndipo imapindulitsa wamoyo aliyense pansi pano.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 7:11
13 Mawu Ofanana  

Koma nzeru, idzapezeka kuti? Ndi luntha, malo ake ali kuti?


Chilamulo cha pakamwa panu chindikomera koposa golide ndi siliva zikwizikwi.


Korona wa anzeru ndi chuma chao; utsiru wa opusa ndiwo utsiru.


pakuti malonda a nzeru aposa malonda a siliva, phindu lake liposa golide woyengeka.


Mtengo wake uposa ngale; ndipo zonse zikukondweretsa sizilingana naye.


Indetu kuunika nkokoma, maso napeza bwino m'kuona dzuwa.


Pamenepo ndinazindikira kuti nzeru ipambana utsiru kwambiri, monga kuunika kupambana mdima.


Usanene, Kodi bwanji masiku akale anapambana ano? Pakuti sulikufunsa mwanzeru pamenepo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa