Mlaliki 7:10 - Buku Lopatulika10 Usanene, Kodi bwanji masiku akale anapambana ano? Pakuti sulikufunsa mwanzeru pamenepo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Usanene, Kodi bwanji masiku akale anapambana ano? Pakuti sulikufunsa mwanzeru pamenepo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Usamafunsa kuti, “Chifukwa chiyani masiku amakedzana anali abwino kupambana masiku ano?” Limeneli si funso lanzeru. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Usamafunse kuti, “Nʼchifukwa chiyani masiku amakedzana anali abwino kupambana masiku ano?” pakuti si chinthu chanzeru kufunsa mafunso oterewa. Onani mutuwo |