Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 5:12 - Buku Lopatulika

12 Tulo ta munthu wogwira ntchito ntabwino, ngakhale adya pang'ono ngakhale zambiri; koma kukhuta kwa wolemera sikumgonetsa tulo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Tulo ta munthu wogwira ntchito ntabwino, ngakhale adya pang'ono ngakhale zambiri; koma kukhuta kwa wolemera sikumgonetsa tulo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Wantchito amagona tulo tabwino, ngakhale adye pang'ono kapena kudya kwambiri. Koma wolemera, chuma sichimgonetsa tulo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Wantchito amagona tulo tabwino ngakhale adye pangʼono kapena kudya kwambiri, koma munthu wolemera, chuma sichimulola kuti agone.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 5:12
4 Mawu Ofanana  

Kuli chabe kwa inu kulawirira mamawa ndi kusagonerapo madzulo, kudya mkate wosautsa kuupeza; kuli tero kuti izi apatsa okondedwa ake ngati m'tulo.


Ndi mtendere ndidzagona pansi, pomwepo ndidzagona tulo; chifukwa Inu, Yehova, mundikhalitsa ine, ndikhale bwino.


Ukagona, sudzachita mantha; udzagona tulo tokondweretsa.


Pamenepo ndinauka, ndinaona; ndipo tulo tanga tinandizunira ine.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa