Mlaliki 4:9 - Buku Lopatulika9 Awiri aposa mmodzi; pakuti ali ndi mphotho yabwino m'ntchito zao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Awiri aposa mmodzi; pakuti ali ndi mphotho yabwino m'ntchito zao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Kukhala aŵiri nkwabwino koposa kukhala wekha, chifukwa ntchito ya anthu aŵiri ili ndi phindu lopambana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Kukhala awiri nʼkwabwino kuposa kukhala wekha, chifukwa ntchito ya anthu awiri ili ndi phindu: Onani mutuwo |