Mlaliki 4:10 - Buku Lopatulika10 Pakuti akagwa, wina adzautsa mnzake; koma tsoka wakugwa wopanda womnyamutsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Pakuti akagwa, wina adzautsa mnzake; koma tsoka wakugwa wopanda womnyamutsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Aŵiriwo akagwa, wina adzautsa mnzake. Koma tsoka amene ali yekha: akagwa, ndiye kuti zavuta, chifukwa palibe wina womuutsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ngati winayo agwa, mnzakeyo adzamudzutsa. Koma tsoka kwa munthu amene agwa ndipo alibe wina woti amudzutse! Onani mutuwo |