Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 4:11 - Buku Lopatulika

11 Ndiponso awiri akagona limodzi afunditsana; koma mmodzi pa yekha kodi adzafunditsidwa bwanji?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndiponso awiri akagona limodzi afunditsana; koma mmodzi pa yekha kodi adzafunditsidwa bwanji?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Ndiponso aŵiri akagona pamodzi amafunditsana. Koma nanga mmodzi angathe kudzifunditsa bwanji?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Komanso ngati anthu awiri agona malo amodzi, adzafunditsana. Koma nanga mmodzi angadzifunditse yekha?

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 4:11
3 Mawu Ofanana  

Pakuti akagwa, wina adzautsa mnzake; koma tsoka wakugwa wopanda womnyamutsa.


Ndipo wina akamgonjetsa mmodziyo, awiri adzachilimika; ndipo chingwe cha nkhosi zitatu sichiduka msanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa