Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 4:5 - Buku Lopatulika

5 Chitsiru chimanga manja ake, ndipo chidya nyama yakeyake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Chitsiru chimanga manja ake, nichidya nyama yakeyake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Paja akuti chitsiru chimangoti manja khodobala, nkumasoŵa chakudya mpaka kumafa ndi njala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Chitsiru chimangoti manja ake lobodo ndi kudzipha chokha ndi njala.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 4:5
10 Mawu Ofanana  

Ndilumirenji mnofu wanga pamano panga, ndi kupereka moyo wanga m'dzanja langa?


Wachifundo achitira moyo wake zokoma; koma wankhanza avuta nyama yake.


Waulesi samaotcha nyama yake anaigwira; koma wolungama amalandira chuma chopambana cha anthu.


Moyo wa waulesi ukhumba osalandira kanthu; koma moyo wa akhama udzalemera.


Waulesi salima chifukwa cha chisanu; adzapemphapempha m'masika osalandira kanthu.


Udzagona mpaka liti, waulesi iwe? Udzauka kutulo tako liti?


Mau a m'kamwa mwa munthu wanzeru nga chisomo; koma milomo ya chitsiru idzachimeza.


Ndipo wina adzakwatula ndi dzanja lamanja, nakhala ndi njala; ndipo adzadya ndi dzanja lamanzere, osakhutai; iwo adzadya munthu yense nyama ya mkono wake wa iye mwini.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa