Mlaliki 4:6 - Buku Lopatulika6 Dzanja limodzi lodzala pali mtendere liposa manja awiri oti thoo pali vuto ndi kungosautsa mtima. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Dzanja limodzi lodzala pali mtendere liposa manja awiri oti thoo pali vuto ndi kungosautsa mtima. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Komabe nkwabwino kukhala ndi moyo wabata wodzaza dzanja limodzi, kupambana kutekeseka ndi ntchito zolemetsa zodzaza manja aŵiri, ndipo kuyesa kuzimvetsa nkungozivuta chabe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Nʼkwabwino kukhala ndi dzanja limodzi lodzaza uli pa mtendere, kuposa kukhala ndi manja awiri odzaza uli pa mavuto, ndipo uku nʼkungodzivuta chabe. Onani mutuwo |