Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 4:3 - Buku Lopatulika

3 inde yemwe sanabadwe konse aposa onse awiriwo popeza sanaone ntchito yoipa yochitidwa kunja kuno.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 inde yemwe sanabadwe konse aposa onse awiriwo popeza sanaone ntchito yoipa yochitidwa kunja kuno.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Koma wopambana onsewo ndi amene sadabadwe nkomwe, ndipo ntchito zoipa zimene zimachitika pansi pano sadaziwone.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Koma wopambana onsewa ndi amene sanabadwe, amene sanaone zoyipa zimene chimachitika pansi pano.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 4:3
11 Mawu Ofanana  

wakusekerera ndi chimwemwe ndi kukondwera pakupeza manda?


Ndaona ntchito zonse zipangidwa kunja kuno; ndipo zonsezo ndi chabe ndi kungosautsa mtima.


Chifukwa chake ndinada moyo; pakuti ntchito azipanga kunja kuno zindisautsa; pakuti zonse ndi chabe ndi kungosautsa mtima.


Koma tsoka ali nalo iwo akukhala ndi pakati, ndi akuyamwitsa ana m'masiku awo!


Chifukwa taonani masiku alinkudza, pamene adzati, Odala ali ouma ndi mimba yosabala, ndi mawere osayamwitsa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa