Mlaliki 4:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo ndinatama akufa atatha kufa kupambana amoyo omwe alipobe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo ndinatama akufa atatha kufa kupambana amoyo omwe alipobe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ndinkaganiza kuti akufa aja amene adapita kale ndi amwai kwambiri kupambana amene akadali ndi moyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndipo ndinanena kuti akufa, amene anafa kale, ndi osangalala kuposa amoyo, amene akanalibe ndi moyo. Onani mutuwo |