Mlaliki 3:2 - Buku Lopatulika2 mphindi yakubadwa ndi mphindi yakumwalira; mphindi yakubzala ndi mphindi yakuzula zobzalazo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 mphindi yakubadwa ndi mphindi yakumwalira; mphindi yakubzala ndi mphindi yakuzula zobzalazo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 pali nthaŵi yobadwa ndi nthaŵi yomwalira, pali nthaŵi yobzala ndi nthaŵi yozula zobzalazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Nthawi yobadwa ndi nthawi yomwalira, nthawi yodzala ndi nthawi yokolola. Onani mutuwo |
Ndipo iye anafuula mwa mau a Yehova kutemberera guwa la nsembe, nati, Guwa la nsembe, guwa la nsembe, atero Yehova, Taona mwana adzabadwa m'nyumba ya Davide, dzina lake ndi Yosiya, adzaphera pa iwe ngati nsembe anthu ansembe a misanje, amene alikufukiza zonunkhira pa iwe, nadzatentha pa iwe mafupa a anthu.