Mlaliki 2:9 - Buku Lopatulika9 Ndinakula chikulire kupambana onse anali mu Yerusalemu ndisanabadwe ine; ndipo nzeru yanganso inakhala nanebe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndinakula chikulire kupambana onse anali m'Yerusalemu ndisanabadwe ine; ndipo nzeru yanganso inakhala nanebe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ndidaasanduka munthu wotchuka, nkudzapambana onse amene ankalamulira ku Yerusalemu kale, monsemo nzeru osandichoka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndinali munthu wotchuka kupambana wina aliyense mu Yerusalemu amene analipo ndisanabadwe. Mu zonsezi nzeru zanga zinali nane. Onani mutuwo |