Mlaliki 12:3 - Buku Lopatulika3 tsikulo omwe asunga nyumba adzanthunthumira, amuna olimba nadzawerama, akupera nadzaleka poperewera, omwe ayang'ana pamazenera nadzadetsedwa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 tsikulo omwe asunga nyumba adzanthunthumira, amuna olimba nadzawerama, akupera nadzaleka poperewera, omwe ayang'ana pamazenera nadzadetsedwa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Nthaŵi imeneyo miyendo yako izidzanjenjemera, manja ako adzafooka. Mano ako oŵerengekawo azidzalephera nkutafuna komwe, ndipo maso ako adzayamba kuchita chidima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Nthawi imene manja ako adzanjenjemera, miyendo yako idzafowoka, pamene mano ako adzalephera kutafuna chifukwa ndi owerengeka, ndipo maso ako adzayamba kuchita chidima. Onani mutuwo |