Mlaliki 10:9 - Buku Lopatulika9 Wosendeza miyala adzaphwetekedwa nayo; wowaza nkhuni nadzitema. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Wosendeza miyala adzaphwetekedwa nayo; wowaza nkhuni nadzitema. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Amene amakumba miyala, itha kumpweteka miyalayo. Amene amaŵaza nkhuni, atha kudzipweteka nazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Amene amaphwanya miyala adzapwetekedwa ndi miyalayo; amene amawaza nkhuni adzapwetekedwa nazo. Onani mutuwo |