Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 10:5 - Buku Lopatulika

5 Pali choipa ndachiona pansi pano, ngati kulakwa koyambira ndi mkulu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Pali choipa ndachiona pansi pano, ngati kulakwa koyambira ndi mkulu;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Pansi pano pali choipa china chimene ndachiwona, choipa chake ndi cholakwa chimene amachichita wolamula.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Pali choyipa chimene ndinachiona pansi pano, kulakwitsa kumene kumachokera kwa wolamulira:

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 10:5
10 Mawu Ofanana  

Wopusa sayenera kukhala ndi zinthu zolongosoka; nanga kapolo ayenera kulamulira akalonga kodi?


Posekera olungama pali ulemerero wambiri; koma pouka oipa anthu amabisala.


Ngati mkulu akukwiyira, usasiye malo ako; chifukwa chifatso chipembedza utachimwa kwambiri.


utsiru ukhazikika pamwamba penipeni, ndipo olemera angokhala mwamanyazi.


Ndiponso ndinaona kunja kuno malo akuweruza, komweko kuli zoipa; ndi malo a chilungamo, komweko kuli zoipa.


Ndinabweranso tsono ndi kupenyera nsautso zonse zimachitidwa kunja kuno; ndipo taona, misozi ya otsenderezedwa, koma analibe wakuwatonthoza; ndipo akuwatsendereza anali ndi mphamvu koma iwowa analibe wakuwatonthoza.


Pamenepo ndinabwera ndi kupenyera zachabe kunja kuno.


Pali choipa chovuta ndachiona kunja kuno, ndicho, chuma chilikupweteka eni ake pochikundika;


Pali choipa ndachiona kunja kuno chifalikira mwa anthu,


Ichi ndi choipa m'zonse zichitidwa pansi pano, chakuti kanthu kamodzi kagwera onse; indetu, mtimanso wa ana a anthu wadzala udyo, ndipo misala ili m'mtima wao akali ndi moyo, ndi pamenepo apita kwa akufa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa