Mlaliki 10:4 - Buku Lopatulika4 Ngati mkulu akukwiyira, usasiye malo ako; chifukwa chifatso chipembedza utachimwa kwambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ngati mkulu akukwiyira, usasiye malo ako; chifukwa chifatso chipembedza utachimwa kwambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Wolamula akakukwiyira, usachoke pa ntchito yako, pakuti kufatsa kumakonza ngakhale zolakwa zazikulu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ngati wolamulira akukwiyira, usachoke pa ntchito yako; kufatsa kumakonza zolakwa zazikulu. Onani mutuwo |