Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 10:3 - Buku Lopatulika

3 Inde, poyendanso chitsiru panjira, nzeru yake imthera ndipo angoti kwa onse kuti, Ndine chitsiru.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Inde, poyendanso chitsiru panjira, nzeru yake imthera ndipo angoti kwa onse kuti, Ndine chitsiru.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Chitsiru ngakhale chikamayenda mu mseu, zochita zake nzopanda nzeru ndithu, ndipo aliyense amachizindikira kuti nchitsirudi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Chitsiru ngakhale chikamayenda mu msewu, zochita zake ndi zopanda nzeru ndipo chimaonetsa aliyense kuti icho ndi chitsirudi.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 10:3
5 Mawu Ofanana  

Yense wochenjera amachita mwanzeru; koma wopusa aonetsa utsiru.


Wopusa sakondwera ndi kuzindikira; koma kungovumbulutsa za m'mtima mwake.


Milomo ya wopusa ifikitsa makangano; ndipo m'kamwa mwake muputa kukwapulidwa.


Pakuti loto lafika mwakuchuluka ntchito; ndipo mau a chitsiru mwakuchuluka maneno.


m'menemo ayesa nchachilendo kuti simuthamanga nao kufikira kusefukira komwe kwa chitayiko, nakuchitirani mwano;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa