Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 10:2 - Buku Lopatulika

2 Wanzeru, mtima wake uli kudzanja lake lamanja; koma chitsiru, mtima wake kulamanzere.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Wanzeru, mtima wake uli kudzanja lake lamanja; koma chitsiru, mtima wake kulamanzere.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Mtima wa munthu wanzeru umamtsogolera bwino, koma mtima wa munthu wopusa umamsokeza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Mtima wa munthu wanzeru umamutsogolera bwino, koma mtima wa munthu wopusa umamusocheretsa.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 10:2
11 Mawu Ofanana  

Nzeru ya wochenjera ndiyo yakuti azindikire njira yake; koma utsiru wa opusa ndiwo chinyengo.


Milomo ya anzeru iwanditsa nzeru, koma mtima wa opusa suli wolungama.


Kodi bwanji mtengo wogulira nzeru uli m'dzanja la chitsiru, popeza wopusa alibe mtima?


Chitsulo chikakhala chosathwa, ndipo ukaleka kunola, uzipambana kulimbikira; koma nzeru ipindulira pochenjeza.


Chitsiru chichulukitsanso mau; koma munthu sadziwa chimene chidzaoneka; ndipo ndani angamuuze chomwe chidzakhala m'tsogolo mwake?


Chilichonse dzanja lako lichipeza kuchichita, uchichite ndi mphamvu yako; pakuti mulibe ntchito ngakhale kulingirira ngakhale kudziwa, ngakhale nzeru, kumanda ulikupitako.


nadzakhalitsa nkhosa kudzanja lake lamanja, koma mbuzi kulamanzere.


Koma muyambe mwafuna Ufumu wake ndi chilungamo chake, ndipo zonse zimenezo zidzaonjezedwa kwa inu.


Chifukwa chake ngati munaukitsidwa pamodzi ndi Khristu, funani zakumwamba, kumene kuli Khristu wokhala padzanja lamanja la Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa