Mlaliki 1:8 - Buku Lopatulika8 Zinthu zonse zilemetsa; munthu sangathe kuzifotokoza; maso sakhuta m'kuona, ndi makutu sakhuta m'kumva. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Zinthu zonse zilemetsa; munthu sakhoza kuzifotokoza; maso sakhuta m'kuona, ndi makutu sakhuta m'kumva. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Zinthu zonse nzolemetsa, kulemera kwake nkosasimbika. Maso sakhuta nkupenya, makutunso sakhuta nkumva. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Zinthu zonse ndi zotopetsa, kutopetsa kwake ndi kosaneneka. Maso satopa ndi kuona kapena khutu kukwaniritsidwa ndi kumva. Onani mutuwo |