Mlaliki 1:7 - Buku Lopatulika7 Mitsinje yonse ithira m'nyanja, koma nyanja yosadzala; komwe imukira mitsinjeyo, komweko ibweranso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Mitsinje yonse ithira m'nyanja, koma nyanja yosadzala; komwe imukira mitsinjeyo, komweko ibweranso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Mitsinje yonse imakathira ku nyanja, koma nyanjayo osadzaza. Kumene madzi adachokera amabwereranso komweko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mitsinje yonse imakathira ku nyanja, koma nyanjayo sidzaza; kumene madziwo amachokera, amabwereranso komweko. Onani mutuwo |