Mlaliki 1:5 - Buku Lopatulika5 Inde dzuwa lituluka, nililowa, nilifulumira komwe linatulukako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Inde dzuwa lituluka, nililowa, nilifulumira komwe linatulukako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Dzuŵa limatuluka, nkukaloŵa, ndipo limapita mwamsanga kumene linatulukira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Dzuwa limatuluka ndipo dzuwa limalowa ndipo limapita mwamsanga kumene limatulukira. Onani mutuwo |