Mlaliki 1:4 - Buku Lopatulika4 Mbadwo wina upita, mbadwo wina nufika; koma dziko lingokhalabe masiku onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Mbadwo wina upita, mbadwo wina nufika; koma dziko lingokhalabe masiku onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mbadwo wina ukutha, wina ukudza, koma dziko lapansi limakhalapobe losasinthika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mibado imabwera ndipo mibado imapita, koma dziko lapansi limakhalapobe nthawi zonse. Onani mutuwo |