Mika 7:4 - Buku Lopatulika4 Wokoma wa iwo akunga mitungwi; woongoka wao aipa koposa mpanda waminga; tsiku la alonda ako la kulangidwa kwako lafika, tsopano kwafika kuthedwa nzeru kwao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Wokoma wa iwo akunga mitungwi; woongoka wao aipa koposa mpanda waminga; tsiku la alonda ako la kulangidwa kwako lafika, tsopano kwafika kuthedwa nzeru kwao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Munthu wabwino koposa ali ngati lunguzi, wolungama koposa ndi wolasa ngati tchinga laminga. Lafika tsiku la chilango, limene alonda ao, aneneri, adanena. Lafika tsiku la chisokonezo chao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Munthu wabwino kwambiri pakati pawo ali ngati mtengo waminga, munthu wolungama kwambiri pakati pawo ndi woyipa kuposa mpanda waminga. Tsiku limene alonda ako ananena lafika, tsiku limene Mulungu akukuchezera. Tsopano ndi nthawi ya chisokonezo chawo. Onani mutuwo |