Mika 7:2 - Buku Lopatulika2 Watha wachifundo m'dziko, palibe woongoka mwa anthu; onsewo alalira mwazi; yense asaka mbale wake ndi ukonde. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Watha wachifundo m'dziko, palibe woongoka mwa anthu; onsewo alalira mwazi; yense asaka mbale wake ndi ukonde. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Anthu abwino atha pa dziko lapansi, palibe ndi mmodzi yemwe wolungama. Onse akubisalirana mwachiwembu. Aliyense akusakira mbale wake mu ukonde. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Anthu opembedza atha mʼdziko; palibe wolungama ndi mmodzi yemwe amene watsala. Anthu onse akubisalirana kuti aphane; aliyense akusaka mʼbale wake ndi khoka. Onani mutuwo |