Mika 7:19 - Buku Lopatulika19 Adzabwera, nadzatichitira nsoni; adzagonjetsa mphulupulu zathu; ndipo mudzataya zochimwa zao zonse m'nyanja yakuya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Adzabwera, nadzatichitira nsoni; adzagonjetsa mphulupulu zathu; ndipo mudzataya zochimwa zao zonse m'nyanja yakuya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Mudzatichitiranso chifundo. Mudzapondereza pansi zolakwa zathu, mudzataya machimo athu onse pansi pa nyanja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Inu mudzatichitiranso chifundo; mudzapondereza pansi machimo athu ndi kuponyera zolakwa zathu zonse pansi pa nyanja. Onani mutuwo |