Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mika 7:15 - Buku Lopatulika

15 Monga masiku a kutuluka kwako m'dziko la Ejipito ndidzamuonetsa zodabwitsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Monga masiku a kutuluka kwako m'dziko la Ejipito ndidzamuonetsa zodabwitsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Chauta akuti, “Ndidzaŵaonetsa zodabwitsa, monga masiku amene ankatuluka ku Ejipito.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 “Ndidzawaonetsa zodabwitsa zanga, ngati masiku amene ndinawatulutsa mʼdziko la Igupto.”

Onani mutuwo Koperani




Mika 7:15
9 Mawu Ofanana  

Ambuye anati, Ndidzawatenganso ku Basani, ndidzawatenganso kozama kwa nyanja,


Ndipo ndidzatambasula dzanja langa, ndi kukantha Aejipito ndi zozizwa zanga zonse ndizichita pakati pake; ndi pambuyo pake adzakulolani kumuka.


Ndipo Iye anati, Taona, Ine ndichita pangano; ndidzachita zozizwa pamaso pa anthu ako onse, sizinachitike zotere ku dziko lonse lapansi, kapena ku mtundu uliwonse wa anthu; ndipo anthu onse amene uli pakati pao adzaona ntchito ya Yehova, pakuti chinthu ndikuchitirachi nchoopsa.


Ndipo padzakhala khwalala la anthu ake otsala ochokera ku Asiriya; monga lija la Israele tsiku lokwera iwo kutuluka m'dziko la Ejipito.


Kodi si ndiwe amene unaumitsa nyanja, madzi akuya kwambiri; anasandutsa nyanja zikhale njira ya kupitapo oomboledwa?


Galamuka, galamuka, khala ndi mphamvu, mkono wa Yehova; galamuka monga masiku akale, mibadwo ya nthawi zakale. Kodi si ndiwe amene unadula Rahabu zipinjirizipinjiri; amene unapyoza chinjoka chamnyanja chija?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa