Mika 7:12 - Buku Lopatulika12 Tsiku lomwelo adzadza kwa iwe, kuchokera ku Asiriya ndi mizinda ya ku Ejipito, kuyambira ku Ejipito kufikira ku Mtsinje, ndi kuyambira kunyanja kufikira kunyanja, ndi kuyambira kuphiri kufikira kuphiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Tsiku lomwelo adzadza kwa iwe, kuchokera ku Asiriya ndi midzi ya ku Ejipito, kuyambira ku Ejipito kufikira ku Mtsinje, ndi kuyambira kunyanja kufikira kunyanja, ndi kuyambira kuphiri kufikira kuphiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Nthaŵi imeneyo anthu anu adzabwerera kwa inu kuchokera ku Asiriya mpaka ku Ejipito, kuchokera ku Ejipito mpaka ku Mtsinje wa Yufurate, ndiponso kuchokera ku nyanja ina mpaka ku nyanja inanso, kuchokera ku phiri lina mpaka ku phiri linanso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Nthawi imeneyo anthu adzabwera kwa inu kuchokera ku Asiriya ndi mizinda ya ku Igupto, ngakhale kuchokera ku Igupto mpaka ku Yufurate ndiponso kuchokera ku nyanja ina mpaka ku nyanja inanso kuchokera ku phiri lina mpaka ku phiri linanso. Onani mutuwo |