Mika 5:9 - Buku Lopatulika9 Dzanja lako likwezeke pamwamba pa iwo akuyambana nawe, ndi adani ako onse aonongeke. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Dzanja lako likwezeke pamwamba pa iwo akuyambana nawe, ndi adani ako onse aonongeke. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Inu Aisraele, mudzapambana adani anu, ndipo adani anu onsewo adzaonongeka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mudzagonjetsa adani anu, ndipo adani anu onse adzawonongeka. Onani mutuwo |