Mika 5:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo kudzachitika tsiku ilo, ati Yehova, ndidzaononga akavalo ako m'kati mwako, ndi kutha magaleta ako; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo kudzachitika tsiku ilo, ati Yehova, ndidzaononga akavalo ako m'kati mwako, ndi kutha magaleta ako; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Komabe Chauta akuuza Aisraele kuti, “Pa tsiku limenelo ndidzaononga akavalo anu onse, ndipo ndidzaphwasula magaleta anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Yehova akuti, “Tsiku limenelo ndidzawononga akavalo anu onse ndi kuphwasula magaleta anu. Onani mutuwo |