Mika 5:11 - Buku Lopatulika11 ndipo ndidzaononga mizinda ya m'dziko lako, ndi kupasula malinga ako onse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 ndipo ndidzaononga midzi ya m'dziko lako, ndi kupasula malinga ako onse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Ndidzaononga mizinda ya m'dziko mwanu ndi kugwetseratu malinga anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ndidzawononga mizinda ya mʼdziko mwanu ndi kugwetsa malinga anu onse. Onani mutuwo |