Mika 3:9 - Buku Lopatulika9 Tamvanitu ichi, akulu a nyumba ya Yakobo inu, ndi oweruza a nyumba ya Israele inu, akuipidwa nacho chiweruzo, ndi kupotoza zoongoka zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Tamvanitu ichi, akulu a nyumba ya Yakobo inu, ndi oweruza a nyumba ya Israele inu, akuipidwa nacho chiweruzo, ndi kupotoza zoongoka zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Imvani izi inu atsogoleri a banja la Yakobe, inu olamulira a banja la Israele. Inu mumadana ndi chilungamo, mumakhotetsa zinthu zokhoza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Imvani izi, inu atsogoleri a nyumba ya Yakobo, inu olamulira nyumba ya Israeli, inu amene mumadana ndi kuweruza kolungama; ndipo mumakhotetsa zinthu zonse zolondola; Onani mutuwo |