Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mika 3:10 - Buku Lopatulika

10 Amanga Ziyoni ndi mwazi, ndi Yerusalemu ndi chisalungamo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Amanga Ziyoni ndi mwazi, ndi Yerusalemu ndi chisalungamo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Mumamanga Ziyoni ndi chuma chochipata pakupha anthu, Yerusalemu mumammanga ndi kuipa kwanu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 inu amene mukumanga Ziyoni pokhetsa magazi, ndi Yerusalemu ndi kuyipa kwanu.

Onani mutuwo Koperani




Mika 3:10
8 Mawu Ofanana  

Nuziti, Atero Ambuye Yehova, Ndiwo mzinda wokhetsa mwazi pakati pake kuti nthawi yake ifike, nudzipangire mafano udzidetsa nao.


Watha wachifundo m'dziko, palibe woongoka mwa anthu; onsewo alalira mwazi; yense asaka mbale wake ndi ukonde.


Akalonga ake m'kati mwake ndiwo mikango yobangula; oweruza ake ndi mimbulu ya madzulo, sasiya kanthu ka mawa.


Ndipo anthu onse anavomereza, ndi kuti, Mwazi wake uli pa ife ndi pa ana athu.


kapena simuganiza kuti nkokoma kwa inu kuti munthu mmodzi afere anthu, ndi kuti mtundu wonse usaonongeke.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa