Mika 1:14 - Buku Lopatulika14 Chifukwa chake pereka mphatso zolawirana kwa Moreseti-Gati; nyumba za Akizibu zidzakhala chinthu chabodza kwa mafumu a Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Chifukwa chake pereka mphatso zolawirana kwa Moreseti-Gati; nyumba za Akizibu zidzakhala chinthu chabodza kwa mafumu a Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono a ku Moreseti-Gati mutsazikane nawo. Anthu a ku Akizibu adzanamiza mafumu a ku Israele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Chifukwa chake perekani mphatso zolawirana ndi a ku Moreseti Gati. Mzinda wa Akizibu udzaonetsa kunama kwa mafumu a Israeli. Onani mutuwo |