Mika 1:15 - Buku Lopatulika15 Ndidzakutengeranso wokhala mu Maresa iwe, iye amene adzakulandira ukhale cholowa chake; ulemerero wa Israele udzafikira ku Adulamu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndidzakutengeranso wokhala m'Maresa iwe, iye amene adzakulandira ukhale cholowa chake; ulemerero wa Israele udzafikira ku Adulamu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Inunso anthu a ku Maresa, ndidzakutumirani adani kuti akugonjetseni. Akuluakulu a ku Israele adzabisala m'thanthwe la Adulamu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ndidzabweretsa mgonjetsi kudzalimbana ndi inu okhala mu Maresa. Ulemerero wa Israeli udzafika ku Adulamu. Onani mutuwo |