Mateyu 9:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Yesu, pozindikira maganizo ao, anati, Chifukwa chanji mulinkuganizira zoipa m'mitima yanu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Yesu, pozindikira maganizo ao, anati, Chifukwa chanji mulinkuganizira zoipa m'mitima yanu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma Yesu adaadziŵa zimene iwo ankaganiza, motero adaŵafunsa kuti, “Bwanji mukuganiza zoipa mumtima mwanu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ndipo podziwa maganizo awo Yesu anati, “Bwanji mukuganiza zoyipa mʼmitima mwanu? Onani mutuwo |