Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 9:31 - Buku Lopatulika

31 Koma iwo anatulukamo, nabukitsa mbiri yake m'dziko lonselo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 Koma iwo anatulukamo, nabukitsa mbiri yake m'dziko lonselo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 Koma iwo adachoka pamenepo nkumakawanditsa mbiri yake ku dera lonselo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 Koma iwo anatuluka mʼnyumbamo nafalitsa za Iye mʼchigawo chonse.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 9:31
11 Mawu Ofanana  

Nthawi imeneyo Herode mfumu anamva mbiri ya Yesu,


Ndipo iwo analandira ndalamazo, nachita monga anawalangiza: ndipo mbiri iyo inabuka mwa Ayuda, kufikira lero lomwe.


Ndipo mbiri yake inabuka ku Siriya konse: ndipo anatengera kwa Iye onse akudwala, ogwidwa ndi nthenda ndi mazunzo a mitundumitundu, ndi ogwidwa ndi ziwanda, ndi akhunyu, ndi amanjenje; ndipo Iye anawachiritsa.


Ndipo mbiri yake imene inabuka m'dziko lonse limenelo.


Ndipo mbiri yake inabuka pompaja kudziko lonse la Galileya lozungulirapo.


Ndipo anawalamulira kuti asauze munthu aliyense; koma monga momwe Iye anawalamulitsa momwenso makamaka analalikira kopambana.


Ndipo Yesu anabwera ndi mphamvu ya Mzimu ku Galileya; ndipo mbiri yake ya Iye inabuka ku dziko lonse loyandikira.


Ndipo mbiri yake ya Iye inafalikira kumalo onse a dziko loyandikira.


Koma makamaka mbiri yake ya Iye inabuka: ndipo mipingo yambiri ya anthu inasonkhana kudzamvera, ndi kudzachiritsidwa nthenda zao.


Ndipo mbiri yake imeneyo inabuka ku Yudeya yense, ndi ku dziko lonse loyandikira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa