Mateyu 9:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo maso ao anaphenyuka. Ndipo Yesu anawauzitsa iwo, nanena, Yang'anirani, asadziwe munthu aliyense. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo maso ao anaphenyuka. Ndipo Yesu anawauzitsa iwo, nanena, Yang'anirani, asadziwe munthu aliyense. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Pamenepo maso ao adaphenyuka. Tsono Yesu adaŵalamula mwamphamvu kuti, “Wina aliyense asazidziŵetu zimenezi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ndipo anayamba kuona. Yesu anawachenjeza kwambiri nati, “Onani, wina aliyense asadziwe za zimenezi.” Onani mutuwo |