Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 9:32 - Buku Lopatulika

32 Ndipo pamene iwo analikutuluka, onani, anabwera naye kwa Iye munthu wosalankhula, wogwidwa ndi chiwanda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Ndipo pamene iwo analikutuluka, onani, anabwera naye kwa Iye munthu wosalankhula, wogwidwa ndi chiwanda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Pamene iwowo ankatuluka m'nyumbamo, anthu ena adabwera kwa Yesu ndi munthu wosatha kulankhula, chifukwa chogwidwa ndi mzimu woipa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Pamene iwo ankatuluka kunja, anthu anabwera kwa Iye ndi munthu wogwidwa ndi mzimu wosayankhula.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 9:32
5 Mawu Ofanana  

Pamenepo wopunduka adzatumpha ngati nswala, ndi lilime la wosalankhula lidzaimba; pakuti m'chipululu madzi adzatuluka, ndi mitsinje m'dziko loti see.


Ndipo mbiri yake inabuka ku Siriya konse: ndipo anatengera kwa Iye onse akudwala, ogwidwa ndi nthenda ndi mazunzo a mitundumitundu, ndi ogwidwa ndi ziwanda, ndi akhunyu, ndi amanjenje; ndipo Iye anawachiritsa.


Ndipo analikutulutsa chiwanda chosalankhula. Ndipo kunali, chitatuluka chiwanda, wosalankhulayo analankhula; ndipo makamu a anthu anazizwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa