Mateyu 8:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Yesu ananena naye, Ndifika Ine, ndidzamchiritsa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Yesu ananena naye, Ndifika Ine, ndidzamchiritsa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Yesu adamuuza kuti, “Chabwino, ndibwera kudzamchiritsa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ndipo Yesu anati kwa iye, “Ine ndibwera kudzamuchiritsa.” Onani mutuwo |