Mateyu 8:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo onani, mzinda wonse unatulukira kukakumana naye Yesu, ndipo m'mene anamuona Iye, anampempha kuti achoke m'malire ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo onani, mudzi wonse unatulukira kukakumana naye Yesu, ndipo m'mene anamuona Iye, anampempha kuti achoke m'malire ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Pamenepo anthu onse amumzindamo adatuluka kuti akakumane ndi Yesu. Tsono atampeza, adamupempha kuti achoke ku dera laolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Ndipo anthu onse a mʼmudziwo anatuluka kukakumana ndi Yesu. Ndipo atamuona Iye, anamupempha kuti achoke mʼdera lawo. Onani mutuwo |