Mateyu 8:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo Yesu, poona makamu ambiri a anthu akumzungulira Iye, analamulira ophunzira amuke kutsidya lina. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo Yesu, poona makamu ambiri a anthu akumzungulira Iye, analamulira ophunzira amuke kutsidya lina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pamene Yesu adaona chinamtindi cha anthu amene adaamuzinga, adauza ophunzira ake kuti, “Tiyeni tiwolokere tsidya linalo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Yesu ataona gulu la anthu litamuzungulira, analamula kuti awolokere kutsidya lina la nyanja. Onani mutuwo |