Mateyu 8:17 - Buku Lopatulika17 kotero kuti chikwaniridwe chonenedwa ndi Yesaya mneneri, kuti, Iye yekha anatenga zofooka zathu, nanyamula nthenda zathu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 kotero kuti chikwaniridwe chonenedwa ndi Yesaya mneneri, kuti, Iye yekha anatenga zofooka zathu, nanyamula nthenda zathu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Adachita zimenezi kuti zipherezere zimene mneneri Yesaya adaanena zakuti, “Iye adatenga zofooka zathu, adasenza nthenda zathu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Uku kunali kukwaniritsa zimene ananena mneneri Yesaya kuti, “Iye anatenga zofowoka zathu, nanyamula nthenda zathu.” Onani mutuwo |