Mateyu 8:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo pakutsika pake paphiripo, inamtsata mipingo yambiri ya anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo pakutsika pake paphiripo, inamtsata mipingo yambiri ya anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Yesu atatsika kuphiri kuja, anthu ambirimbiri adamtsatira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Iye atatsika ku phiri kuja, anthu ambirimbiri anamutsata. Onani mutuwo |