Mateyu 7:9 - Buku Lopatulika9 Kapena munthu ndani wa inu, amene pompempha mwana wake mkate, adzampatsa mwala? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Kapena munthu ndani wa inu, amene pompempha mwana wake mkate, adzampatsa mwala? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ndani mwa inu, mwana wake atampempha buledi, iye nkumupatsa mwala? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Ndani mwa inu, mwana wake akamupempha buledi amamupatsa mwala? Onani mutuwo |