Mateyu 7:10 - Buku Lopatulika10 Kapena pompempha nsomba, adzampatsa iye njoka kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Kapena pompempha nsomba, adzampatsa iye njoka kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Kapena atampempha nsomba, iye nkumupatsa njoka? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Kapena ngati mwana apempha nsomba, kodi amamupatsa njoka? Onani mutuwo |