Mateyu 7:18 - Buku Lopatulika18 Sungathe mtengo wabwino kupatsa zipatso zoipa, kapena mtengo wamphuchi kupatsa zipatso zokoma. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Sungathe mtengo wabwino kupatsa zipatso zoipa, kapena mtengo wamphuchi kupatsa zipatso zokoma. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Mtengo wabwino sungabale zipatso zoipa, kapena mtengo woipa kubala zipatso zabwino ai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mtengo wabwino sungabale chipatso choyipa, ndi mtengo woyipa sungabale chipatso chabwino. Onani mutuwo |