Mateyu 6:9 - Buku Lopatulika9 Chifukwa chake pempherani inu chomwechi: Atate wathu wa Kumwamba, Dzina lanu liyeretsedwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Chifukwa chake pempherani inu chomwechi: Atate wathu wa Kumwamba, Dzina lanu liyeretsedwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Nchifukwa chake popemphera muziti, “Atate athu akumwamba, dzina lanu lilemekezedwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Chifukwa chake pempherani motere: “ ‘Atate athu akumwamba, dzina lanu lilemekezedwe, Onani mutuwo |