Mateyu 6:34 - Buku Lopatulika34 Chifukwa chake musadere nkhawa za mawa; pakuti mawa adzadzidera nkhawa iwo okha. Zikwanire tsiku zovuta zake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Chifukwa chake musadere nkhawa za mawa; pakuti mawa adzadzidera nkhawa iwo okha. Zikwanire tsiku zovuta zake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Motero musadere nkhaŵa zamaŵa. Zamaŵa nzamaŵa. Tsiku lililonse lili ndi zovuta zake zokwanira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Chifukwa chake musadere nkhawa ndi za mawa, popeza tsiku lililonse lili ndi zovuta zake zokwanira. Onani mutuwo |